This song is about coming back to Jesus again for renewal after wandering away from Him. Along the Journey, we can become distracted by the things of this world and lose sight of our Heavenly destination.
lyrics
Lyrics:
Verse 1:
Ndili nkudza kwa inu Yesu wanga. (I am coming to you my Jesus.)
Ndisauka, ndinachimwa ine. (I suffer, I sinned.)
Ndinakonda zamdzikoli. (I loved the things of this world.)
Ndinakayesa mzopindulitsa, mbuye. (I thought they were valuable, Lord.)
Koma zonse ndizachabe, mbuye. (But all are useless, Lord.)
Mapetonso nchionongeko. (The end is also destruction.)
Ine ntchito zanga ndalephela ine. (My work fails me.)
Ndingo pempha mkhale ndine (I just ask be with me.)
Mbuye, ndili nkudza kwa inu (Lord, I am coming to you)
Yesu wanga. (my Jesus.)
Mundikonzenso (Renew me again.)
Ndinachimwa – Ine mundikonze ine. (I sinned – You cleanse me.)
Yo! Ooh mama.
Verse 2:
Moyo wanga ufanana, mbuye (My life is similar, Lord)
Ndi Nkhosa yotaika. (to the lost sheep.)
Ine pakuona nkhondo, (I see the wars,)
Njala, nthenda mdziko. (hunger, diseases in the world.)
Moyo wanga, uli ndi mantha mbuye. (My life, it has fear, Lord.)
Ndifooka ndi zoipa zanga, (I am weak with my wickedness)
Ndi ndinayesa kuzikonza ine. (and I tried to cleanse myself.)
Ndapeza mphamvu ndilibe. (I found myself powerless.)
credits
from Nyimbo Za Paulendo (Songs for the Journey),
released December 4, 2014
Lyrics by Daniel Lymon (AEC Chilomoni Choirmaster)
Sung by AEC Chilomoni Youth Choir
Produced by Richard Mphopheya
Modular synths sparkle amidst piano, vibes, and other organic instruments stringing together constellations of sound. Bandcamp New & Notable Sep 22, 2023