1. |
||||
"The LORD will keep you from all harm -
he will watch over your life;
the LORD will watch over your coming and going
both now and forevermore."
- Psalm 121:8 (NIV)
|
||||
2. |
||||
Lyrics:
Yesu ndi ndodo yoyendera. (Jesus in the staff for travelling)
Yesu ndi ndodo yoyendera.
Yesu ndi ndodo yoyendera.
Yesu ndi khomo yolowera. (Jesus is the Door for entering through)
Yesu ndi khomo yolowera (x2).
Yesu ndi khomo… ooh
Yesu ndi khomo yolowera (x2).
Yesu ndi njira yoyendamo …ooh. (Jesus is the Way for walking on)
Yesu ndi njira
Yesu ndi njira yoyendamo
Yesu ndi njira yoyendamo (x2).
|
||||
3. |
||||
Lyrics:
Mulungu wathu ndinu wachifundo (Our God He is merciful)
Chikondi chanu mchosaneneka (His love indescribable)
Mwatisunga tonsefe ndi moyo (He sustains us all with life)
Kufikira tsiku ili lalero. (To this very day.)
M’mene dziko!!! (As the World!!!)
M’mene dziko lavutilamu (As the World is so troubled)
Wina kumangokhalabe osalapa (Still others are living in sin without repentance)
M’mene anthu akuferamu (As people are dying)
Inu kumangokhalabe osalapa. (You are living in sin without repentance.)
Ngozi zonze (All calamities)
Ngozi zonse zachitikazi (All calamities have happened)
Wina kumangokhalabe osalapa. (Still others are living in sin without repentance.)
Nanga mukuchedweranji amai, abambo? (Why are you delaying mothers, fathers?)
Mukuchedweranji mnyamata, msungwana? (Why are you delaying sons, daughters?)
Chikuchedweranji? Lapani, lapani. (Why the delay? Repent, repent.)
Panthaka apa papitatu anthu. (In this soil, people have gone.)
Anzeru zawo ambiri apita. (Many of the wise have also gone.)
Azipembedzo zambiri apita (Many of the religious have also gone.)
Tangosala mwina, inu ndi ine. (We are remaining, you and me.)
|
||||
4. |
Thanthwe Langa (My Rock)
06:13
|
|||
Lyrics:
Thanthwe langa ndi Yesu. (My rock is Jesus.)
M’bale wanga, thanthwe ilo, (My brother, that rock,)
Thanthwe langa ndi Yesu. (My rock is Jesus.)
Timanyamuka maulendo athu, (We start off our journeys,)
Opita uko kutali. (Of going far away.)
Posakhalitsa ife timabwerera. (Soon we return.)
Kubwerera komwe tachoka. (Returning where we left.)
Koma ulendo ulendo wapafupi, (But the journey, the short journey,)
Wopita uko kumanda. (of going to the grave.)
Wopita kumeneko bwanji samabwerera? (Those going there, why don’t they return?)
M’bale wanga uzifunse. (My brother, ask yourself.)
Eee Konzeka! (Be prepared!)
Konzeka ndi ulendowu. (Be prepared for this journey.)
Lapa tchimo ulindi moyo. (Repent while you are alive.)
M’manja mopanda kanthu ine. (Nothing in my hands.)
Mtanda ndingogwiradi. (The Cross I cling.)
Maliseke mbuye mundimveke. (Nakedness, Lord, clothe me.)
Ndili ndekha sungeni. (I’m all alone, keep me.)
Moyo wanga uvutika. (My life is troubled.)
Nkaganiza zatsikulo, (If I think of that Day,)
Mmene ndizaona mbuye Yesu. (When I will see my Lord Jesus.)
Ali kuweluza dziko. (Judging the World.)
|
||||
5. |
||||
Lyrics:
Sindibwerera kwa Lusifala ine. (I am not returning to Lucifer.)
Sindibwerera kwa Lusifala ine. (I am not returning to Lucifer.)
Ndalima mtima ulendo kwa Tate. (I am bold for the journey to the Father)
Ndalimba mtima (x2). (I am bold)
Sindibwerera… (I am not returning…)
Sindibwerera kwa Lusifala ine. (I am not returning to Lucifer.)
Ndalima mtima ulendo kwa Tate (x2). (I am bold for the journey to the Father)
Anandimenya kwawo kwa Farawo. (He has hit me at Pharaoh’s land)
Anandikhomera misomali mmanja. (He has nailed my hands)
Ndalima mtima ulendo kwa Tate (x2). (I am bold for the journey to the Father)
Katundu wanga ndanyamula. (My belongings I have carried)
Ndalima mtima ulendo kwa Tate (x2). (I am bold for the journey to the Father)
Adani anga ondidziwa ine. (My enemies have known me.)
Ndalima mtima ulendo kwa Tate (x2). (I am bold for the journey to the Father)
Sindibwerera kwa Lusifala ine. (I am not returning to Lucifer.)
Ndalima mtima ulendo kwa Tate (x2). (I am bold for the journey to the Father)
|
||||
6. |
||||
Lyrics:
Verse 1:
Ndili nkudza kwa inu Yesu wanga. (I am coming to you my Jesus.)
Ndisauka, ndinachimwa ine. (I suffer, I sinned.)
Ndinakonda zamdzikoli. (I loved the things of this world.)
Ndinakayesa mzopindulitsa, mbuye. (I thought they were valuable, Lord.)
Koma zonse ndizachabe, mbuye. (But all are useless, Lord.)
Mapetonso nchionongeko. (The end is also destruction.)
Ine ntchito zanga ndalephela ine. (My work fails me.)
Ndingo pempha mkhale ndine (I just ask be with me.)
Chorus:
Mbuyee! Inu! Mbuye wanga. (Lord! You! My Lord.)
Mundikonze ine. (Cleanse me.)
Ooh! Mama!
Mbuye, ndili nkudza kwa inu (Lord, I am coming to you)
Yesu wanga. (my Jesus.)
Mundikonzenso (Renew me again.)
Ndinachimwa – Ine mundikonze ine. (I sinned – You cleanse me.)
Yo! Ooh mama.
Verse 2:
Moyo wanga ufanana, mbuye (My life is similar, Lord)
Ndi Nkhosa yotaika. (to the lost sheep.)
Ine pakuona nkhondo, (I see the wars,)
Njala, nthenda mdziko. (hunger, diseases in the world.)
Moyo wanga, uli ndi mantha mbuye. (My life, it has fear, Lord.)
Ndifooka ndi zoipa zanga, (I am weak with my wickedness)
Ndi ndinayesa kuzikonza ine. (and I tried to cleanse myself.)
Ndapeza mphamvu ndilibe. (I found myself powerless.)
|
||||
7. |
||||
Lyrics:
Ndiyenda kuuinka. (I walk in the light)
Ndiyenda kuuinka. (I walk in the light)
Ndiyenda pamapazi Ambuyeyo (x2). (I walk at the foot of the Lord)
Akabwera tidzamka nawo. (When He comes we will go with Him)
Chikondi chithetsa mantha. (Love ends fear)
Ndiyenda kuunika. (I walk in the light)
Woipa akanyodola. (Evil gossip)
Chikondi chithetsa mantha. (Love ends fear)
Ndiyenda kuunika. (I walk in the light)
Mbendera yanga ili njoowooh. (My flag it is upright)
Chikondi chithetsa mantha. (Love ends fear)
|
||||
8. |
||||
Lyrics:
Pilira nawoni mavuto. (Persevere in troubles.)
Ngakhale padzikoli tikuvutika. (Although in this world we are troubled.)
Tisabwezere choipa kwa wochita zoipa, (Let us not repay evil with evil,)
Zabwino kwa wochita zoipa (x2). (Good with evil.)
Yembekeza. Yembekeza. (Wait. Wait.)
Pilira nawo, mbale, ye… (Persevere in troubles, my brothers, ye…)
Yembekeza-Yembekeza-Yembekeza-Yembekeza. (Wait-Wait-Wait-Wait.)
Ayehova m’busa wanga. (Jehovah, my shepherd.)
Pilira nawo mbale wanga. (Persevere, my brothers)
Usanene ndizabwezera choipa kwa wochita zoipa (x2). (Don’t say I will repay evil with evil.)
Ayehova m’busa wanga. (Jehovah, my shepherd.)
Pilira nawo mbale wanga. (Persevere, my brothers)
Masiku akusadziwa Yehova, (In the days of not knowing Jehovah,)
Iye analekerera zintchito zathu, (He allowed our doings,)
Pakuti Yesuyo anakwera kumwamba, (However, Jesus has ascended to heaven,)
Zabwino kwa wochita zoipa (x2). (Good over evil).
|
||||
9. |
||||
Lyrics:
Dziko lapansi ndi dziko loipa. (The world is a world of evil.)
Lampachika Yesu mwana wa Mulungu, (Crucified Jesus Son of God,)
Mwana wa Mulungu analibe tchimo (Sinless Son of God.)
Dziko lapansi ndi dziko loipa. (The world is a world of evil.)
Chorus:
Kudzakhala… (There will be…)
Woooh chikondwerero (Woooh great celebration)
Kudzakhala… (There will be…)
Woooh chikondwerero (Woooh great celebration)
Pobwera Yesu (When Jesus comes)
Woooh chikondwerero (Woooh great celebration)
Popita M’mwamba (As we’re going to heaven)
Woooh chikondwerero (Woooh great celebration)
Mwana wa Mulungu, pobwera m’dzikoli, (Son of God, came to this earth,)
Cholinga chake tikapulumuke (His purpose is for us to be saved)
Anthu a m’dzikoli anamukana Yesu (People of this earth rejected Jesus)
Dziko lapansi ndi dziko loipa. (The world is a world of evil.)
|
||||
10. |
Wodala (Blessed)
04:46
|
|||
Lyrics:
Verse 1:
Kweza maso kumapiri Kuli Yehova. (Look up to the hills, there is Jehovah.)
Zamdziko m’bale wanga ndizachabe. (Things of the world, my brother, are not worthy.)
Mvela mau akunena mokuchenjeza. (Listen to the words of warning.)
Ma peto amoyo wako ndichiweluzo. (The end of your life is judgement.)
Chorus:
Odala! (Blessed!)
Odala ndiamene wapeza Yesu. (Blessed in the one who has found Jesus.)
Chifukwa adzauona ufumu wake. (Because they will see his kingdom.)
Verse 2:
Iwe, nzanga ganizira zamoyo wako. (You, my friend, think about your life.)
Pakuti sudziwa za tsiku ilo. (Since you don’t know the Day.)
Ona nkhondo njala, (See the wars, the hunger,)
Nthenda paliponse. (the diseases everywhere.)
Zonsezi zisonyeza kutha kwa dziko. (All these show the end of the World.)
|
||||
11. |
||||
"Praise the LORD, all you servants of the LORD
Who minister by night in the house of the LORD."
-Psalm 134:1 (NIV)
|
Streaming and Download help
If you like AEC Youth, you may also like:
Bandcamp Daily your guide to the world of Bandcamp