This song is about God's mercy and sustaining love towards those who journey with Him despite the troubled world in which we live. It's also a call to people to repent while they can and not delay.
lyrics
Lyrics:
Mulungu wathu ndinu wachifundo (Our God He is merciful)
Chikondi chanu mchosaneneka (His love indescribable)
Mwatisunga tonsefe ndi moyo (He sustains us all with life)
Kufikira tsiku ili lalero. (To this very day.)
M’mene dziko!!! (As the World!!!)
M’mene dziko lavutilamu (As the World is so troubled)
Wina kumangokhalabe osalapa (Still others are living in sin without repentance)
M’mene anthu akuferamu (As people are dying)
Inu kumangokhalabe osalapa. (You are living in sin without repentance.)
Ngozi zonze (All calamities)
Ngozi zonse zachitikazi (All calamities have happened)
Wina kumangokhalabe osalapa. (Still others are living in sin without repentance.)
Nanga mukuchedweranji amai, abambo? (Why are you delaying mothers, fathers?)
Mukuchedweranji mnyamata, msungwana? (Why are you delaying sons, daughters?)
Chikuchedweranji? Lapani, lapani. (Why the delay? Repent, repent.)
Panthaka apa papitatu anthu. (In this soil, people have gone.)
Anzeru zawo ambiri apita. (Many of the wise have also gone.)
Azipembedzo zambiri apita (Many of the religious have also gone.)
Tangosala mwina, inu ndi ine. (We are remaining, you and me.)
credits
from Nyimbo Za Paulendo (Songs for the Journey),
released December 4, 2014
Lyrics by AEC Bangwe Youth Choir
Sung by AEC Bangwe Youth Choir
Produced by Richard Mphopheya
Modular synths sparkle amidst piano, vibes, and other organic instruments stringing together constellations of sound. Bandcamp New & Notable Sep 22, 2023